Ekisodo 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mose anali atauza akuluwo kuti: “Tidikireni pompano mpaka titabwerako.+ Panotu muli ndi Aroni ndi Hura.+ Aliyense amene ali ndi mlandu wofuna kuweruzidwa afikire iwowa.”+
14 Koma Mose anali atauza akuluwo kuti: “Tidikireni pompano mpaka titabwerako.+ Panotu muli ndi Aroni ndi Hura.+ Aliyense amene ali ndi mlandu wofuna kuweruzidwa afikire iwowa.”+