Deuteronomo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Yehova anayamba kukulankhulani kuchokera pakati pa moto.+ Inu munamva mawu koma simunaone kalikonse.+ Munangomva mawu osaona kalikonse.+ Deuteronomo 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anakuchititsani kumva mawu ake kuchokera kumwamba n’cholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuona moto wake woopsa, ndipo munamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+ Machitidwe 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Uyu ndi amene+ anali pakati pa mpingo+ m’chipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu komanso makolo athu paphiri la Sinai. Pamenepo analandira mawu opatulika+ omwe ndi amphamvu kuti awapereke kwa inu.
12 Pamenepo Yehova anayamba kukulankhulani kuchokera pakati pa moto.+ Inu munamva mawu koma simunaone kalikonse.+ Munangomva mawu osaona kalikonse.+
36 Anakuchititsani kumva mawu ake kuchokera kumwamba n’cholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuona moto wake woopsa, ndipo munamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+
38 Uyu ndi amene+ anali pakati pa mpingo+ m’chipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu komanso makolo athu paphiri la Sinai. Pamenepo analandira mawu opatulika+ omwe ndi amphamvu kuti awapereke kwa inu.