Luka 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.”
16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.”