Levitiko 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atatero, moto unatsika kuchokera kwa Yehova ndi kuwawononga,+ moti anafa pamaso pa Yehova.+ 2 Samueli 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo mkwiyo wa Yehova+ unayakira Uza ndipo Mulungu woona anamukantha+ pomwepo chifukwa cha kuchita chinthu chosalemekeza Mulungu chimenechi. Moti Uza anafera pomwepo, pafupi ndi likasa la Mulungu woona.+
7 Pamenepo mkwiyo wa Yehova+ unayakira Uza ndipo Mulungu woona anamukantha+ pomwepo chifukwa cha kuchita chinthu chosalemekeza Mulungu chimenechi. Moti Uza anafera pomwepo, pafupi ndi likasa la Mulungu woona.+