Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+

  • Yoswa 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Dzuka! Yeretsa anthuwa,+ uwauze kuti, ‘Mawa mudziyeretse, pakuti Yehova, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Kalanga Isiraeli, pakati panu pali zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Anthu inu simudzathanso kulimbana ndi adani anu, kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.

  • 1 Samueli 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye anayankha kuti: “Inde, n’kwabwino. Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova. Dziyeretseni,+ ndipo mupite nane kopereka nsembe.” Chotero iye anayeretsa Jese ndi ana ake, kenako anawaitanira kopereka nsembe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena