Amosi 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tsopano zinthu zofanana ndi zimenezi ndi zimene ndidzakuchitira, iwe Isiraeli. Ndipo chifukwa chakuti ndidzakuchitira zimenezi, konzekera kukumana ndi Mulungu wako,+ iwe Isiraeli.
12 “Tsopano zinthu zofanana ndi zimenezi ndi zimene ndidzakuchitira, iwe Isiraeli. Ndipo chifukwa chakuti ndidzakuchitira zimenezi, konzekera kukumana ndi Mulungu wako,+ iwe Isiraeli.