1 Samueli 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma wansembeyo anayankha Davide kuti: “Ndilibe mkate wamba, koma pali mkate wopatulika.+ Nditha kukupatsa umenewu ngati anyamatawo ayesetsa kudzisunga osagona ndi akazi.”+ 1 Akorinto 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musamanane,+ kupatulapo ngati mwagwirizana kuimitsa kaye mangawawo kwa nthawi yodziwika,+ kuti muthere nthawi pa kupemphera, kenako mukhalenso mwa nthawi zonse, kuopera kuti Satana angapitirize kumakuyesani+ mukalephera kudzigwira.+
4 Koma wansembeyo anayankha Davide kuti: “Ndilibe mkate wamba, koma pali mkate wopatulika.+ Nditha kukupatsa umenewu ngati anyamatawo ayesetsa kudzisunga osagona ndi akazi.”+
5 Musamanane,+ kupatulapo ngati mwagwirizana kuimitsa kaye mangawawo kwa nthawi yodziwika,+ kuti muthere nthawi pa kupemphera, kenako mukhalenso mwa nthawi zonse, kuopera kuti Satana angapitirize kumakuyesani+ mukalephera kudzigwira.+