Nehemiya 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno munatsikira paphiri la Sinai+ ndi kulankhula nawo muli kumwamba.+ Munawapatsa zigamulo zowongoka+ ndi malamulo a choonadi,+ mfundo zabwino ndi malangizo abwino.+ Salimo 81:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi ya nsautso unaitana ndipo ine ndinakupulumutsa.+Ndinayamba kukuyankha m’malo obisika a bingu.+Ndinakusanthula pamadzi a Meriba.+ [Seʹlah.]
13 Ndiyeno munatsikira paphiri la Sinai+ ndi kulankhula nawo muli kumwamba.+ Munawapatsa zigamulo zowongoka+ ndi malamulo a choonadi,+ mfundo zabwino ndi malangizo abwino.+
7 Pa nthawi ya nsautso unaitana ndipo ine ndinakupulumutsa.+Ndinayamba kukuyankha m’malo obisika a bingu.+Ndinakusanthula pamadzi a Meriba.+ [Seʹlah.]