Machitidwe 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti sindinakubisireni kanthu, koma ndinakuuzani chifuniro+ chonse cha Mulungu.