Salimo 81:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,+Amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.+Tsegulani pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+ Hoseya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Panalibe Mulungu wina amene unali kumudziwa kupatulapo ine. Panalibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.+ Aroma 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi salinso Mulungu wa anthu a mitundu ina?+ Inde, iye alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina,+
10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,+Amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.+Tsegulani pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+
4 “Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Panalibe Mulungu wina amene unali kumudziwa kupatulapo ine. Panalibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.+
29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi salinso Mulungu wa anthu a mitundu ina?+ Inde, iye alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina,+