Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Yakobo anauza anthu a m’banja lake ndi onse amene anali naye kuti: “Chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu.+ Dziyeretseni ndipo sinthani zovala zanu.+

  • Ekisodo 23:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Usaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo usapange chilichonse chofanana ndi zifaniziro zawo,+ koma uzigwetse ndithu ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+

  • 1 Akorinto 10:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ayi, koma ndikunena kuti zinthu zimene mitundu ina imapereka nsembe imazipereka kwa ziwanda,+ osati kwa Mulungu, ndipo sindikufuna kuti mukhale ogawana ndi ziwanda.+

  • 1 Yohane 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Inu ana okondedwa, pewani mafano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena