Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo,* chifukwa cha zolakwa za anthu odana ndi ine.+

  • 2 Samueli 21:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 mutipatse ana ake aamuna 7,+ ndipo tionetse+ mitembo yawo kwa Yehova mwa kuipachika ku Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, munthu amene Yehova+ anamusankha kukhala mfumu.” Pamenepo mfumu inati: “Ndiwapereka m’manja mwanu.”

  • 1 Mafumu 21:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga?+ Popeza wadzichepetsa chifukwa cha ine, sindidzabweretsa tsokali m’masiku ake.+ M’malomwake, ndidzalibweretsa panyumba yake m’masiku a mwana wake.”+

  • Mateyu 23:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 kuti magazi onse olungama okhetsedwa padziko lapansi abwere pa inu,+ kuyambira magazi a Abele+ wolungama+ mpaka magazi a Zekariya mwana wa Barakiya, amene inu munamupha pakati pa nyumba yopatulika ndi guwa lansembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena