Levitiko 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wonyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Khamu lonse lizim’ponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.+ Deuteronomo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Usagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wako mosasamala,+ pakuti Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina lake mosasamala osam’langa.+ Yoswa 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tiwasiya kuti akhale ndi moyo, kuti Mulungu asatikwiyire chifukwa cha lumbiro limene tinawalumbirira.”+
16 Wonyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Khamu lonse lizim’ponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.+
11 “‘Usagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wako mosasamala,+ pakuti Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina lake mosasamala osam’langa.+
20 Tiwasiya kuti akhale ndi moyo, kuti Mulungu asatikwiyire chifukwa cha lumbiro limene tinawalumbirira.”+