-
Deuteronomo 5:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wako.+ Usagwire ntchito iliyonse,+ iweyo kapena mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, kapolo wako wamwamuna, kapolo wako wamkazi, ng’ombe yako yamphongo, bulu wako, chiweto chako chilichonse, kapena mlendo wokhala mumzinda wanu,+ kuti nayenso kapolo wako wamwamuna ndi kapolo wako wamkazi, azipumula monga iwe.+
-