Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Nditaona+ chovala chamtengo wapatali cha ku Sinara,+ pakati pa katundu wotsalayo, chokongola m’maonekedwe, komanso masekeli* a siliva 200, ndi mtanda umodzi wa golide wolemera masekeli 50, ndinazikhumba zinthuzo,+ ndipo ndinazitenga.+ Panopo chovalacho ndinachikumbira pansi, pakati pa hema wanga, pamodzi ndi ndalamazo, ndipo ndalamazo zili pansi pa chovalacho.”+

  • Mika 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+

  • Luka 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Khalani maso ndipo chenjerani ndi kusirira kwa nsanje kwamtundu uliwonse,+ chifukwa ngakhale munthu atakhala ndi zochuluka chotani, moyo wake suchokera m’zinthu zimene ali nazo.”+

  • Aroma 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiye tinene kuti chiyani? Kodi Chilamulo ndi uchimo?+ Ayi m’pang’ono pomwe! Kunena zoona, sindikanadziwa uchimo+ zikanakhala kuti panalibe Chilamulo. Ndiponso, mwachitsanzo, sindikanadziwa kusirira kwa nsanje+ zikanakhala kuti Chilamulo sichinanene kuti: “Usasirire mwansanje.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena