Deuteronomo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndinaima pakati pa Yehova ndi inu pa nthawi imeneyo,+ kuti ndikuuzeni mawu a Yehova, (pakuti munali kuopa moto, ndipo simunakwere m’phirimo).+ Pamenepo iye anati, Salimo 97:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+
5 Ine ndinaima pakati pa Yehova ndi inu pa nthawi imeneyo,+ kuti ndikuuzeni mawu a Yehova, (pakuti munali kuopa moto, ndipo simunakwere m’phirimo).+ Pamenepo iye anati, Salimo 97:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+
2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+