Deuteronomo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Koma kapoloyo akakuuza kuti, ‘Ine sindikusiyani!’ chifukwa chakuti amakukonda komanso amakonda banja lako, popeza unali kukhala naye bwino,+
16 “Koma kapoloyo akakuuza kuti, ‘Ine sindikusiyani!’ chifukwa chakuti amakukonda komanso amakonda banja lako, popeza unali kukhala naye bwino,+