Deuteronomo 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 uzitenga choboolera ndi kuboola khutu lake ali pakhomo, mpaka chobooleracho chigunde chitseko ndipo azikhala kapolo wako moyo wake wonse.+ Uzichitanso zimenezi ndi kapolo wako wamkazi.
17 uzitenga choboolera ndi kuboola khutu lake ali pakhomo, mpaka chobooleracho chigunde chitseko ndipo azikhala kapolo wako moyo wake wonse.+ Uzichitanso zimenezi ndi kapolo wako wamkazi.