Aefeso 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 pakuti palibe munthu anadapo thupi lake, koma amalidyetsa ndi kulikonda,+ mmenenso Khristu amachitira ndi mpingo, 1 Timoteyo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithudi, ngati munthu sasamalira anthu amene ndi udindo wake kuwasamalira,+ makamaka a m’banja lake,+ wakana+ chikhulupiriro+ ndipo ndi woipa kuposa munthu wosakhulupirira.
29 pakuti palibe munthu anadapo thupi lake, koma amalidyetsa ndi kulikonda,+ mmenenso Khristu amachitira ndi mpingo,
8 Ndithudi, ngati munthu sasamalira anthu amene ndi udindo wake kuwasamalira,+ makamaka a m’banja lake,+ wakana+ chikhulupiriro+ ndipo ndi woipa kuposa munthu wosakhulupirira.