Salimo 139:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Maso anu anandiona pamene ndinali mluza,+Ndipo ziwalo zanga zonse zinalembedwa m’buku lanu.M’bukumo munalembamo za masiku amene zinapangidwa+Koma panalibe ngakhale chiwalo chimodzi chimene chinali chitapangidwa. Yeremiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.”
16 Maso anu anandiona pamene ndinali mluza,+Ndipo ziwalo zanga zonse zinalembedwa m’buku lanu.M’bukumo munalembamo za masiku amene zinapangidwa+Koma panalibe ngakhale chiwalo chimodzi chimene chinali chitapangidwa.
5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.”