Aefeso 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu ambuye, muzichitiranso akapolo anu chimodzimodzi ndipo muleke kuwaopseza,+ pakuti mukudziwa kuti Ambuye wa nonsenu, wa iwowo ndi wa inuyo,+ ali kumwamba ndipo alibe tsankho.+ Akolose 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu anthu amene muli ambuye, pitirizani kuchitira akapolo+ anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, podziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+
9 Inu ambuye, muzichitiranso akapolo anu chimodzimodzi ndipo muleke kuwaopseza,+ pakuti mukudziwa kuti Ambuye wa nonsenu, wa iwowo ndi wa inuyo,+ ali kumwamba ndipo alibe tsankho.+
4 Inu anthu amene muli ambuye, pitirizani kuchitira akapolo+ anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, podziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+