Genesis 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuwonjezera pamenepo, ndidzafunsa za magazi anu. Ngati magazi anu akhetsedwa ndi chamoyo chilichonse, chamoyocho chiyenera kuphedwa, ndipo ngati moyo wa munthu wachotsedwa ndi munthu mnzake ndidzaufuna kuchokera kwa iye.+ Numeri 35:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “‘Musadetse dziko+ limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndiwo amadetsa dziko. Ndipo dziko lodetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe mwa njira ina, koma ndi magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+
5 Kuwonjezera pamenepo, ndidzafunsa za magazi anu. Ngati magazi anu akhetsedwa ndi chamoyo chilichonse, chamoyocho chiyenera kuphedwa, ndipo ngati moyo wa munthu wachotsedwa ndi munthu mnzake ndidzaufuna kuchokera kwa iye.+
33 “‘Musadetse dziko+ limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndiwo amadetsa dziko. Ndipo dziko lodetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe mwa njira ina, koma ndi magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+