Zekariya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako ndinawauza kuti: “Ngati mukuona kuti n’zoyenera,+ ndipatseni malipiro anga, koma ngati mukuona kuti n’zosayenera musandipatse.” Pamenepo iwo anandipatsa ndalama 30 zasiliva monga malipiro anga.+ Mateyu 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri Yeremiya* zinakwaniritsidwa. Iye anati: “Ndipo anatenga ndalama 30 zasiliva,+ zomwe zinali mtengo wogulira munthu umene ena mwa ana a Isiraeli anamuikira,
12 Kenako ndinawauza kuti: “Ngati mukuona kuti n’zoyenera,+ ndipatseni malipiro anga, koma ngati mukuona kuti n’zosayenera musandipatse.” Pamenepo iwo anandipatsa ndalama 30 zasiliva monga malipiro anga.+
9 Pamenepo zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri Yeremiya* zinakwaniritsidwa. Iye anati: “Ndipo anatenga ndalama 30 zasiliva,+ zomwe zinali mtengo wogulira munthu umene ena mwa ana a Isiraeli anamuikira,