Mateyu 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iye anawayankha kuti: “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa imodzi, ndiyeno nkhosayo n’kugwera m’dzenje+ tsiku la sabata, sangaigwire ndi kuitulutsa?+ 1 Akorinto 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Aliyense asamangodzifunira zopindulitsa iye yekha basi,+ koma zopindulitsanso wina.+
11 Koma iye anawayankha kuti: “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa imodzi, ndiyeno nkhosayo n’kugwera m’dzenje+ tsiku la sabata, sangaigwire ndi kuitulutsa?+