Deuteronomo 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ukaona bulu wa m’bale wako kapena ng’ombe yake itagwa pamsewu usailekerere. Uzim’thandiza m’bale wako mwa kuidzutsa.+ Luka 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Koma inu amene mukumvetseranu ine ndikukuuzani kuti, Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kuchita zabwino+ kwa amene akudana nanu. Aroma 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musalole kuti choipa chikugonjetseni, koma pitirizani kugonjetsa choipa mwa kuchita chabwino.+
4 “Ukaona bulu wa m’bale wako kapena ng’ombe yake itagwa pamsewu usailekerere. Uzim’thandiza m’bale wako mwa kuidzutsa.+
27 “Koma inu amene mukumvetseranu ine ndikukuuzani kuti, Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kuchita zabwino+ kwa amene akudana nanu.