Levitiko 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kwa zaka 6 muzilima minda yanu, ndipo m’zaka 6 zomwezo muzidulira mitengo yanu ya mpesa ndi kukolola mbewu zanu.+
3 Kwa zaka 6 muzilima minda yanu, ndipo m’zaka 6 zomwezo muzidulira mitengo yanu ya mpesa ndi kukolola mbewu zanu.+