Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Koma khalani tcheru ndipo musamale moyo wanu,+ kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona,+ ndi kuti mitima yanu isaiwale zinthu zimenezo masiku onse a moyo wanu.+ Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauza za zinthu zimenezo,+

  • 1 Timoteyo 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Nthawi zonse uzisamala ndi zimene umachita+ komanso zimene umaphunzitsa.+ Pitiriza kuchita zimenezi, chifukwa ukatero udzadzipulumutsa wekha komanso anthu okumvera.+

  • Aheberi 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pochita zimenezo, muonetsetse kuti wina asalandidwe kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ komanso kuti pakati panu pasatuluke muzu wapoizoni+ woyambitsa mavuto, ndi kuti ambiri asaipitsidwe nawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena