Deuteronomo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+ Yoswa 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+ Hoseya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Sindidzamulola kutchulanso mayina a zifaniziro za Baala,+ ndipo iye sadzakumbukiranso mayina awo.+
3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+
7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+
17 “‘Sindidzamulola kutchulanso mayina a zifaniziro za Baala,+ ndipo iye sadzakumbukiranso mayina awo.+