Levitiko 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 kapena ngati wauzidwa kuti wachimwa mwa kuphwanya lamulo,+ azibweretsa mbuzi yaing’ono yamphongo,+ yopanda chilema, kuti ikhale nsembe yake. Numeri 28:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Komanso muzipereka mwana wa mbuzi wophimbira machimo anu.+
23 kapena ngati wauzidwa kuti wachimwa mwa kuphwanya lamulo,+ azibweretsa mbuzi yaing’ono yamphongo,+ yopanda chilema, kuti ikhale nsembe yake.