Ekisodo 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndipo khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ anapita limodzi ndi ana a Isiraeli. Anapitanso ndi nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zambirimbiri. Numeri 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akongolerenji malo ako okhala Yakobo! Mahema ako n’ngokongola ndithu Isiraeli!+ Zekariya 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse amene akubwera kudzamenyana ndi Yerusalemu,+ azidzapita kukagwadira Mfumu,+ Yehova wa makamu,+ chaka ndi chaka,+ ndi kukachita nawo chikondwerero cha misasa.+
38 Ndipo khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ anapita limodzi ndi ana a Isiraeli. Anapitanso ndi nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zambirimbiri.
16 “Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse amene akubwera kudzamenyana ndi Yerusalemu,+ azidzapita kukagwadira Mfumu,+ Yehova wa makamu,+ chaka ndi chaka,+ ndi kukachita nawo chikondwerero cha misasa.+