Ekisodo 21:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 mwiniwake wa dzenjelo azilipira.+ Malipirowo azipereka kwa mwiniwake wa ng’ombeyo, koma iye azitenga nyama yakufayo. Ekisodo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Munthu akaba ng’ombe kapena nkhosa, n’kuipha kapena kuigulitsa, azilipira ng’ombe zisanu pa ng’ombe imodzi imene waba, ndi nkhosa zinayi pa nkhosa imodzi imene waba.+
34 mwiniwake wa dzenjelo azilipira.+ Malipirowo azipereka kwa mwiniwake wa ng’ombeyo, koma iye azitenga nyama yakufayo.
22 “Munthu akaba ng’ombe kapena nkhosa, n’kuipha kapena kuigulitsa, azilipira ng’ombe zisanu pa ng’ombe imodzi imene waba, ndi nkhosa zinayi pa nkhosa imodzi imene waba.+