-
Levitiko 25:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Koma ngati sanaiwombole chaka chimodzicho chisanathe, nyumba imene ili mumzinda wokhala ndi linga izikhala ya wogulayo mpaka kalekale, m’mibadwo yake yonse, ndipo isabwezedwe m’Chaka cha Ufulu.
-