Levitiko 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+
10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+