Ekisodo 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndipo khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ anapita limodzi ndi ana a Isiraeli. Anapitanso ndi nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zambirimbiri. Yoswa 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno atsogoleriwo anawauza kuti: “Akhale ndi moyo, ndipo akhale otola nkhuni ndi otungira madzi khamu lonse la Isiraeli,+ monga mmene tinawalonjezera.”+
38 Ndipo khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ anapita limodzi ndi ana a Isiraeli. Anapitanso ndi nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zambirimbiri.
21 Ndiyeno atsogoleriwo anawauza kuti: “Akhale ndi moyo, ndipo akhale otola nkhuni ndi otungira madzi khamu lonse la Isiraeli,+ monga mmene tinawalonjezera.”+