Levitiko 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 aziwerenga zaka zimene zapitapo kuchokera pamene anagulitsa malowo, ndipo azibweza ndalama zotsala kwa munthu amene anagula malowo. Akatero azibwerera kumalo akewo.+
27 aziwerenga zaka zimene zapitapo kuchokera pamene anagulitsa malowo, ndipo azibweza ndalama zotsala kwa munthu amene anagula malowo. Akatero azibwerera kumalo akewo.+