Levitiko 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati zaka zimene udzakhala ukukololapo n’zambiri, azikugulitsa pa mtengo wokwera,+ koma ngati zakazo zili zochepa azitsitsa mtengo wa malowo, chifukwa akukugulitsa mbewu zimene udzakhala ukukololapo. Levitiko 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ngati wapereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika m’Chaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake woikidwiratu.+
16 Ngati zaka zimene udzakhala ukukololapo n’zambiri, azikugulitsa pa mtengo wokwera,+ koma ngati zakazo zili zochepa azitsitsa mtengo wa malowo, chifukwa akukugulitsa mbewu zimene udzakhala ukukololapo.
18 Koma ngati wapereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika m’Chaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake woikidwiratu.+