Levitiko 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo wansembe azinena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyamayo ilili, kaya ndi yabwino kapena yoipa. Mtengo wa nyamayo+ umene wansembe wanena uzikhala womwewo. Levitiko 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ngati wapereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika m’Chaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake woikidwiratu.+
12 Ndipo wansembe azinena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyamayo ilili, kaya ndi yabwino kapena yoipa. Mtengo wa nyamayo+ umene wansembe wanena uzikhala womwewo.
18 Koma ngati wapereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika m’Chaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake woikidwiratu.+