Ekisodo 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zimene uzichita ndi mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe ndi wa nkhosa yako ndi izi:+ Azikhala ndi mayi wake masiku 7.+ Pa tsiku la 8 uzim’pereka kwa ine. Deuteronomo 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Mwana aliyense wamphongo woyamba kubadwa wa ng’ombe kapena wa nkhosa uzim’patulira Yehova Mulungu wako.+ Usagwiritse ntchito mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe, kapena kumeta ubweya wa mwana woyamba kubadwa wa nkhosa.+
30 Zimene uzichita ndi mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe ndi wa nkhosa yako ndi izi:+ Azikhala ndi mayi wake masiku 7.+ Pa tsiku la 8 uzim’pereka kwa ine.
19 “Mwana aliyense wamphongo woyamba kubadwa wa ng’ombe kapena wa nkhosa uzim’patulira Yehova Mulungu wako.+ Usagwiritse ntchito mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe, kapena kumeta ubweya wa mwana woyamba kubadwa wa nkhosa.+