-
Levitiko 27:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Asaichotse ndi kuikapo ina, ndipo asasinthanitse yabwino ndi yoipa kapena yoipa ndi yabwino. Koma ngati waisinthanitsa ndi nyama ina, zonse ziwiri, yoyambayo ndiponso imene waisinthanitsa nayo, zizikhala zopatulika.
-