Levitiko 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno wansembe aziphimba machimo+ a munthuyo pamaso pa Yehova, ndipo azikhululukidwa chilichonse mwa zonse zimene angachite zom’palamulitsa.” Levitiko 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma musadye nyama ya nsembe yamachimo imene ena mwa magazi+ ake adzalowa nawo m’chihema chokumanako kuti aphimbire machimo m’malo oyerawo. Imeneyo muziitentha ndi moto.
7 Ndiyeno wansembe aziphimba machimo+ a munthuyo pamaso pa Yehova, ndipo azikhululukidwa chilichonse mwa zonse zimene angachite zom’palamulitsa.”
30 Koma musadye nyama ya nsembe yamachimo imene ena mwa magazi+ ake adzalowa nawo m’chihema chokumanako kuti aphimbire machimo m’malo oyerawo. Imeneyo muziitentha ndi moto.