Genesis 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Potsirizira pake, madzi anamuthera+ m’thumba lachikopa lija, ndipo iye anangomusiya+ mwana uja pachitsamba. Levitiko 13:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 “Koma wansembeyo akaona, n’kupeza kuti nthendayo sinafalikire pachovalacho, m’litali kapena m’lifupi, kapena pa chilichonse chopangidwa ndi chikopa,+ Maliko 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiponso, palibe munthu amene amathira vinyo watsopano m’matumba achikopa akale. Akachita zimenezo, vinyoyo amaphulitsa matumbawo. Kenako vinyoyo amatayika ndipo matumbawo amawonongeka.+ Koma anthu amathira vinyo watsopano m’matumba achikopa atsopano.”+
15 Potsirizira pake, madzi anamuthera+ m’thumba lachikopa lija, ndipo iye anangomusiya+ mwana uja pachitsamba.
53 “Koma wansembeyo akaona, n’kupeza kuti nthendayo sinafalikire pachovalacho, m’litali kapena m’lifupi, kapena pa chilichonse chopangidwa ndi chikopa,+
22 Ndiponso, palibe munthu amene amathira vinyo watsopano m’matumba achikopa akale. Akachita zimenezo, vinyoyo amaphulitsa matumbawo. Kenako vinyoyo amatayika ndipo matumbawo amawonongeka.+ Koma anthu amathira vinyo watsopano m’matumba achikopa atsopano.”+