Levitiko 14:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 wansembe+ azibweranso kudzaiona. Ngati nthendayo yafalikira m’nyumbamo, limenelo ndi khate loopsa.+ Nyumbayo ndi yodetsedwa.
44 wansembe+ azibweranso kudzaiona. Ngati nthendayo yafalikira m’nyumbamo, limenelo ndi khate loopsa.+ Nyumbayo ndi yodetsedwa.