Numeri 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana a Aroni mayina awo anali awa: woyamba anali Nadabu, kenako Abihu,+ Eleazara+ ndi Itamara.+ Malaki 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndakutumizirani lamulo limeneli+ kuti pangano+ limene ndinapangana ndi Levi lipitirire,”+ watero Yehova wa makamu.
4 Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndakutumizirani lamulo limeneli+ kuti pangano+ limene ndinapangana ndi Levi lipitirire,”+ watero Yehova wa makamu.