Levitiko 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Usavule m’bale* wa mayi ako+ ndi mlongo wa bambo ako,+ chifukwa wochita zimenezi wavula wachibale wake.+ Aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.
19 “‘Usavule m’bale* wa mayi ako+ ndi mlongo wa bambo ako,+ chifukwa wochita zimenezi wavula wachibale wake.+ Aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.