Levitiko 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aroni ndi ana ake kuti asayandikire zinthu zopatulika za ana a Isiraeli ndi kuipitsa dzina langa loyera.+ Asayandikire zinthu zimene azipatula kuti azipereke nsembe kwa ine.+ Ine ndine Yehova. Levitiko 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zili choncho kuti ansembe asaipitse zinthu zopatulika za ana a Isiraeli, zimene angapereke kwa Yehova,+
2 “Uza Aroni ndi ana ake kuti asayandikire zinthu zopatulika za ana a Isiraeli ndi kuipitsa dzina langa loyera.+ Asayandikire zinthu zimene azipatula kuti azipereke nsembe kwa ine.+ Ine ndine Yehova.
15 Zili choncho kuti ansembe asaipitse zinthu zopatulika za ana a Isiraeli, zimene angapereke kwa Yehova,+