Ekisodo 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma nyama ya ng’ombeyo, chikopa chake ndi ndowe zake uzitenthe ndi moto kunja kwa msasa.+ Ng’ombeyo ndi nsembe yamachimo. Levitiko 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Koma kunena za chikopa cha ng’ombeyo ndi nyama yake yonse pamodzi ndi mutu wake, ziboda zake, matumbo ake ndi ndowe zake,+
14 Koma nyama ya ng’ombeyo, chikopa chake ndi ndowe zake uzitenthe ndi moto kunja kwa msasa.+ Ng’ombeyo ndi nsembe yamachimo.
11 “‘Koma kunena za chikopa cha ng’ombeyo ndi nyama yake yonse pamodzi ndi mutu wake, ziboda zake, matumbo ake ndi ndowe zake,+