4 wansembe azim’lamula kuti atenge zofunika pa kudziyeretsa kwake. Azitenga mbalame zamoyo ziwiri zosadetsedwa,+ nthambi ya mtengo wa mkungudza,+ ulusi wofiira kwambiri+ ndi kamtengo ka hisope.+
49 Ndiyeno kuti achite mwambo woyeretsa nyumbayo, azitenga mbalame ziwiri,+ nthambi ya mtengo wa mkungudza,+ ulusi wofiira kwambiri+ ndi kamtengo ka hisope.