Levitiko 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso munthu wokhudza bedi lakelo azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+
5 Komanso munthu wokhudza bedi lakelo azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+