Deuteronomo 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova+ kuyambira tsiku limene ndinakudziwani. Salimo 106:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kuwonjezera pamenepo, iwo anaputa mkwiyo pa madzi a ku Meriba,+Moti Mose sizinamuyendere bwino chifukwa cha anthu amenewa.+
32 Kuwonjezera pamenepo, iwo anaputa mkwiyo pa madzi a ku Meriba,+Moti Mose sizinamuyendere bwino chifukwa cha anthu amenewa.+