Numeri 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwo anabwera kwa Mose ndi Aroni, ndiponso kwa khamu lonse la ana a Isiraeli m’chipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera onsewo za ulendo wawo n’kuwaonetsa zipatso za kudzikolo. Numeri 33:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pambuyo pake ananyamuka ku Kadesi, n’kukamanga msasa kuphiri la Hora,+ kumalire ndi dziko la Edomu.
26 Iwo anabwera kwa Mose ndi Aroni, ndiponso kwa khamu lonse la ana a Isiraeli m’chipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera onsewo za ulendo wawo n’kuwaonetsa zipatso za kudzikolo.
37 Pambuyo pake ananyamuka ku Kadesi, n’kukamanga msasa kuphiri la Hora,+ kumalire ndi dziko la Edomu.